Yesaya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yerusalemu wapunthwa ndipo Yuda wagwa,+ chifukwa lilime lawo ndiponso zochita zawo n’zotsutsana ndi Yehova.+ Iwo achita zinthu zomupandukira m’maso ake olemekezeka.+
8 Yerusalemu wapunthwa ndipo Yuda wagwa,+ chifukwa lilime lawo ndiponso zochita zawo n’zotsutsana ndi Yehova.+ Iwo achita zinthu zomupandukira m’maso ake olemekezeka.+