1 Mafumu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno chifaniziro cha ng’ombe chimodzi anakachiika ku Beteli,+ china anakachiika ku Dani.+ Amosi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa.+ Muzichita zolakwa mobwerezabwereza ku Giligala+ ndipo muzibweretsa nsembe zanu m’mawa. Pa tsiku lachitatu, muzibweretsa chakhumi* chanu.+
4 “‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa.+ Muzichita zolakwa mobwerezabwereza ku Giligala+ ndipo muzibweretsa nsembe zanu m’mawa. Pa tsiku lachitatu, muzibweretsa chakhumi* chanu.+