Zefaniya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Gaza adzakhala mzinda wosiyidwa,+ ndipo Asikeloni adzakhala bwinja.+ Kunena za Asidodi,+ anthu ake adzawathamangitsa dzuwa lili paliwombo,+ ndipo Ekironi adzazulidwa.+ Zekariya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzachotsa zinthu zake zamagazi m’kamwa mwake ndipo ndidzachotsa chakudya chake chonyansa pakati pa mano ake.+ Aliyense amene adzatsale adzakhala wa Mulungu wathu. Wotsalayo adzakhala ngati mfumu+ mu Yuda,+ ndipo Ekironi adzakhala ngati Myebusi.+
4 Gaza adzakhala mzinda wosiyidwa,+ ndipo Asikeloni adzakhala bwinja.+ Kunena za Asidodi,+ anthu ake adzawathamangitsa dzuwa lili paliwombo,+ ndipo Ekironi adzazulidwa.+
7 Ndidzachotsa zinthu zake zamagazi m’kamwa mwake ndipo ndidzachotsa chakudya chake chonyansa pakati pa mano ake.+ Aliyense amene adzatsale adzakhala wa Mulungu wathu. Wotsalayo adzakhala ngati mfumu+ mu Yuda,+ ndipo Ekironi adzakhala ngati Myebusi.+