Yeremiya 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehova wanena motsutsana ndi anthu a ku Anatoti+ amene akufuna moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere m’dzina la Yehova,+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.” Amosi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ pakuti ndi malo opatulika a mfumu,+ ndiponso Beteli ndi nyumba ya ufumu uno.”
21 Choncho Yehova wanena motsutsana ndi anthu a ku Anatoti+ amene akufuna moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere m’dzina la Yehova,+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.”
13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ pakuti ndi malo opatulika a mfumu,+ ndiponso Beteli ndi nyumba ya ufumu uno.”