Yesaya 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chipululu ndi malo opanda madzi zidzasangalala.+ Dera lachipululu lidzakondwa ndipo lidzachita maluwa n’kukhala lokongola ngati duwa la safironi.+ Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+
35 Chipululu ndi malo opanda madzi zidzasangalala.+ Dera lachipululu lidzakondwa ndipo lidzachita maluwa n’kukhala lokongola ngati duwa la safironi.+
12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+