Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;

      Ndidzam’penya, koma si panopo.

      Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,

      Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+

      Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+

      Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.

  • Yesaya 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+

  • Yeremiya 48:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Inu mudzagwidwa ndi adani chifukwa mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu.+ Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapolo+ pamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena