Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+

  • Deuteronomo 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene dzanja lanu likuchita.+ Iye akudziwa za kuyenda kwanu kudutsa m’chipululu chachikulu ichi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi,+ ndipo simunasowe kanthu.”’+

  • Nehemiya 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kwa zaka 40+ munawapatsa chakudya m’chipululu. Iwo sanasowe kanthu.+ Zovala zawo sizinathe+ ndipo mapazi awo sanatupe.+

  • Machitidwe 7:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Chotero Mulungu anawaleka+ kuti atumikire makamu akumwamba monga mmene malemba amanenera m’buku la aneneri.+ Malembawo amati, ‘Anthu inu a nyumba ya Isiraeli, kodi m’chipululu muja munali kupereka kwa ine nyama zansembe ndi zopereka zina kwa zaka 40?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena