Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+

  • 1 Mafumu 17:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Eliya+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi+ analankhula ndi Ahabu kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli+ amene ndimam’tumikira,+ sikugwa mame kapena mvula+ zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditalamula.”+

  • 1 Mafumu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chotero Eliya anachoka kumeneko n’kupita kwa Elisa mwana wa Safati, ndipo anam’peza akulima ndi pulawo+ yokokedwa ndi ng’ombe ziwiri zamphongo. Panali mapulawo 12 oterowo ndipo pulawo yake inali kumbuyo kwa onsewo. Choncho Eliya anapita pamene panali Elisa n’kumuponyera chovala chake chauneneri.+

  • 2 Mbiri 36:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wa makolo awo anapitiriza kuwatumizira machenjezo kudzera mwa amithenga ake.+ Anawatumiza mobwerezabwereza chifukwa ankamvera chisoni anthu akewo+ ndiponso malo ake okhala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena