Yesaya 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera pamahatchi n’kuthawa!”+ N’chifukwa chake mudzathawe. Munanenanso kuti: “Tidzakwera pamahatchi othamanga kwambiri!”+ N’chifukwa chake anthu okuthamangitsani adzakhale othamanga kwambiri.+
16 Ndipo munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera pamahatchi n’kuthawa!”+ N’chifukwa chake mudzathawe. Munanenanso kuti: “Tidzakwera pamahatchi othamanga kwambiri!”+ N’chifukwa chake anthu okuthamangitsani adzakhale othamanga kwambiri.+