Yona 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Yona ananyamuka ndi kupita ku Nineve mogwirizana ndi mawu a Yehova.+ Mzinda wa Nineve unali waukulu pamaso pa Mulungu,+ ndipo mtunda wake unali woyenda masiku atatu. Mateyu 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi nawenso sukanam’chitira chifundo+ kapolo mnzako, monga momwe ine ndinakuchitira chifundo?’+
3 Pamenepo Yona ananyamuka ndi kupita ku Nineve mogwirizana ndi mawu a Yehova.+ Mzinda wa Nineve unali waukulu pamaso pa Mulungu,+ ndipo mtunda wake unali woyenda masiku atatu.