Ezara 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira pamenepo, anthu a m’dzikolo anakhala akufooketsa+ manja a anthu a ku Yuda ndi kuwagwetsa ulesi pa ntchito yomanga.+ Ezara 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mawu amene analembedwa m’kalata ya mfumu Aritasasita atawerengedwa pamaso pa Rehumu,+ Simusai+ mlembi, ndi anzawo,+ iwo anapita msangamsanga kwa Ayuda ku Yerusalemu n’kukawaletsa ntchitoyo mwankhondo.+
4 Kuyambira pamenepo, anthu a m’dzikolo anakhala akufooketsa+ manja a anthu a ku Yuda ndi kuwagwetsa ulesi pa ntchito yomanga.+
23 Mawu amene analembedwa m’kalata ya mfumu Aritasasita atawerengedwa pamaso pa Rehumu,+ Simusai+ mlembi, ndi anzawo,+ iwo anapita msangamsanga kwa Ayuda ku Yerusalemu n’kukawaletsa ntchitoyo mwankhondo.+