Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 11:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 ndipo mudzalandira temberero+ limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ n’kupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo, n’kuyamba kutsatira milungu ina imene simukuidziwa.

  • Deuteronomo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+

  • Salimo 109:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye anakonda kutemberera ena,+ mwakuti matemberero anabwera kwa iye.+

      Koma kudalitsa ena sikunali kumusangalatsa,+

      Moti madalitso anali patali ndi iye,+

  • Yesaya 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 N’chifukwa chake temberero lameza dzikolo,+ ndipo anthu okhala m’dzikolo apezeka ndi mlandu. Chotero anthu okhala m’dzikolo achepamo, ndipo anthu amene atsalamo ndi ochepa kwambiri.+

  • Malaki 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana, ndipo adzatembenuza mitima ya ana kuti ikhale ngati ya abambo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena