Oweruza 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi Mulungu sanapereke Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani m’manja mwanu? Ndipo ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unaphwa.+ Mlaliki 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu wa mtsogoleri ukakuukira, usachoke pamalo ako,+ chifukwa kudekha kumachepetsa machimo aakulu.+
3 Kodi Mulungu sanapereke Orebi ndi Zeebi,+ akalonga a Midiyani m’manja mwanu? Ndipo ine ndachita chiyani poyerekeza ndi inu?” Atanena mawu amenewa, mkwiyo wawo unaphwa.+
4 Mzimu wa mtsogoleri ukakuukira, usachoke pamalo ako,+ chifukwa kudekha kumachepetsa machimo aakulu.+