Yesaya 41:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’chipululu ndidzabzalamo mtengo wa mkungudza, mtengo wa mthethe, mtengo wa mchisu, ndi mtengo wamafuta.+ M’dera lachipululu ndidzabzalamo mtengo wofanana ndi mkungudza, mtengo wa ashi,* ndi mtengo wa paini pa nthawi imodzimodziyo.+ Yesaya 55:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’malo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa mkungudza.+ M’malo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu.+ Zimenezi zidzamutchukitsa Yehova,+ ndipo zidzakhala chizindikiro choti sichidzachotsedwa mpaka kalekale.”+
19 M’chipululu ndidzabzalamo mtengo wa mkungudza, mtengo wa mthethe, mtengo wa mchisu, ndi mtengo wamafuta.+ M’dera lachipululu ndidzabzalamo mtengo wofanana ndi mkungudza, mtengo wa ashi,* ndi mtengo wa paini pa nthawi imodzimodziyo.+
13 M’malo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa mkungudza.+ M’malo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu.+ Zimenezi zidzamutchukitsa Yehova,+ ndipo zidzakhala chizindikiro choti sichidzachotsedwa mpaka kalekale.”+