17 chifukwa chakuti andisiya n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho mkwiyo wanga wayakira malo ano ndipo suzimitsidwa.’”’+
6 Choncho ndasonyeza mkwiyo wanga ndi ukali wanga ndipo watentha mizinda ya Yuda ndi misewu ya Yerusalemu.+ Lero malo amenewa ndi owonongeka ndipo asanduka bwinja.’+