Yesaya 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku. Hagai 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Pa tsiku limenelo ndidzakutenga iwe Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli,+ mtumiki wanga,’ watero Yehova. ‘Ndipo ndidzakusunga ngati mphete yodindira,+ chifukwa iwe ndi amene ndakusankha,’+ watero Yehova wa makamu.”+
13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku.
23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Pa tsiku limenelo ndidzakutenga iwe Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli,+ mtumiki wanga,’ watero Yehova. ‘Ndipo ndidzakusunga ngati mphete yodindira,+ chifukwa iwe ndi amene ndakusankha,’+ watero Yehova wa makamu.”+