-
Zekariya 1:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pamenepo ndinafunsa kuti: “Kodi awa abwera kudzachita chiyani?”
Mngeloyo anayankha kuti: “Zimenezi ndi nyanga+ zimene zinabalalitsa Yuda, moti panalibe amene anatha kudzutsa mutu wake. Amisiri awa adzabwera kudzaopseza nyangazi, kudzawononga nyanga za mitundu ina ya anthu imene ikukwezera nyanga* yawo dziko la Yuda kuti ibalalitse anthu ake.”+
-