Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+ Yeremiya 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ndikadzawazula ndidzawachitiranso chifundo+ moti ndidzawabwezeretsa. Ndidzabwezeretsa aliyense pacholowa chake, ndiponso pamalo ake.”+ Hoseya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndidzathetsa kusakhulupirika kwawo.+ Ndidzawakonda mwa kufuna kwanga,+ chifukwa mkwiyo wanga wawachokera.+ Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+
7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+
15 Ndiyeno ndikadzawazula ndidzawachitiranso chifundo+ moti ndidzawabwezeretsa. Ndidzabwezeretsa aliyense pacholowa chake, ndiponso pamalo ake.”+
4 “Ndidzathetsa kusakhulupirika kwawo.+ Ndidzawakonda mwa kufuna kwanga,+ chifukwa mkwiyo wanga wawachokera.+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+