Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Ndiyeno upange mbale zake, zikho, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Uzipange ndi golide woyenga bwino.+

  • Ekisodo 37:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Atatero anapanga ziwiya za patebulolo, mbale zake, zikho zake, mitsuko yake ndi mbale zake zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+

  • Numeri 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Iwo aziyala nsalu yabuluu patebulo+ la mkate wachionetsero, n’kuikapo mbale,+ zikho, mbale zolowa,+ ndi mitsuko ya nsembe yachakumwa. Mkate wachionetsero womwe ndi nsembe ya nthawi zonse+ uzikhalabe pomwepo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena