Salimo 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Onse amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala ndi kukondwera.+Nthawi zonse azinena kuti:+“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pa mtendere.”+
27 Onse amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala ndi kukondwera.+Nthawi zonse azinena kuti:+“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pa mtendere.”+