Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Mateyu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+ Maliko 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwe umadziwa malamulo akuti, ‘Usaphe munthu,*+ Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama,+ Usachite chinyengo+ ndiponso lakuti Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+ Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,”+ ndilo lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo:+
12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+
19 Iwe umadziwa malamulo akuti, ‘Usaphe munthu,*+ Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama,+ Usachite chinyengo+ ndiponso lakuti Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+