Malaki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+ “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’ “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+
7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+ “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’ “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+