Mateyu 13:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 “Ndiponso ufumu wakumwamba uli ngati khoka loponyedwa m’nyanja limene limasonkhanitsa nsomba zamitundumitundu.+
47 “Ndiponso ufumu wakumwamba uli ngati khoka loponyedwa m’nyanja limene limasonkhanitsa nsomba zamitundumitundu.+