Yeremiya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+ Malaki 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu. Luka 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake. Akufuna kuyeretseratu mbee! malo ake opunthirapo mbewu ndi kututira+ tirigu munkhokwe yake. Koma mankhusu+ adzawatentha ndi moto+ umene sungazimitsidwe.”
7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+
4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu.
17 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake. Akufuna kuyeretseratu mbee! malo ake opunthirapo mbewu ndi kututira+ tirigu munkhokwe yake. Koma mankhusu+ adzawatentha ndi moto+ umene sungazimitsidwe.”