Mateyu 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Sizili choncho pakati panu,+ koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+ Maliko 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho anakhala pansi ndi kuitana ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse, ndiponso mtumiki wa onse.”+ Luka 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+
26 Sizili choncho pakati panu,+ koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+
35 Choncho anakhala pansi ndi kuitana ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse, ndiponso mtumiki wa onse.”+
26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamng’ono kwambiri pa nonsenu,+ ndipo amene ali mtsogoleri akhale wotumikira.+