Mateyu 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+ Mateyu 13:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Kenako anawauza kuti: “Popeza kuti zili choncho, mphunzitsi aliyense wa anthu akaphunzitsidwa za ufumu wakumwamba,+ amakhala ngati munthu, mwininyumba, amene amatulutsa zinthu zatsopano ndi zakale mosungiramo chuma chake.”+
41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+
52 Kenako anawauza kuti: “Popeza kuti zili choncho, mphunzitsi aliyense wa anthu akaphunzitsidwa za ufumu wakumwamba,+ amakhala ngati munthu, mwininyumba, amene amatulutsa zinthu zatsopano ndi zakale mosungiramo chuma chake.”+