Salimo 118:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wodala ndi Iye wobwera m’dzina la Yehova.+Takudalitsani anthu inu potuluka m’nyumba ya Yehova.+ Mateyu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+
9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+