Genesis 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+
7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+