Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+ Luka 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokhulupirika pa chinthu chaching’ono alinso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu wosalungama pa chinthu chaching’ono alinso wosalungama pa chinthu chachikulu.+
20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+
10 Munthu wokhulupirika pa chinthu chaching’ono alinso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu wosalungama pa chinthu chaching’ono alinso wosalungama pa chinthu chachikulu.+