Miyambo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+ Luka 12:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndithu ndikukuuzani, Adzamuika kukhala woyang’anira zinthu zake zonse.+
24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+