-
Yohane 11:57Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
57 Apa n’kuti ansembe aakulu ndi Afarisi atalamula kuti aliyense amene angadziwe kumene kuli Yesu, aulule kuti iwo akamugwire.
-