Maliko 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+ Luka 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anavomereza, ndipo anayamba kufunafuna mpata wabwino kuti amupereke kwa iwo popanda khamu la anthu pafupi.+
11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+
6 Choncho iye anavomereza, ndipo anayamba kufunafuna mpata wabwino kuti amupereke kwa iwo popanda khamu la anthu pafupi.+