Maliko 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ophunzirawo anapita ndi kulowa mumzinda, ndipo zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Chotero anakonzekera pasika kumeneko.+ Luka 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ananyamuka ndi kupita. Kumeneko zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Ndipo anakonza pasika kumeneko.+
16 Choncho ophunzirawo anapita ndi kulowa mumzinda, ndipo zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Chotero anakonzekera pasika kumeneko.+
13 Choncho ananyamuka ndi kupita. Kumeneko zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Ndipo anakonza pasika kumeneko.+