Maliko 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chakumadzulo ndithu, Yesu anafika limodzi ndi ophunzira ake 12 aja.+ Luka 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi itakwana, anakhala patebulo la chakudya, atumwi akenso anali naye limodzi.+