Deuteronomo 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘Wotembereredwa ndi munthu wolandira chiphuphu kuti akanthe ndi kupheratu munthu, kuti akhetse magazi a munthu wosachimwa.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Luka 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Mwana wa munthu akuchoka malinga n’zimene zinanenedweratu.+ Koma, tsoka kwa munthu amene akumupereka!”+
25 “‘Wotembereredwa ndi munthu wolandira chiphuphu kuti akanthe ndi kupheratu munthu, kuti akhetse magazi a munthu wosachimwa.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
22 Chifukwa Mwana wa munthu akuchoka malinga n’zimene zinanenedweratu.+ Koma, tsoka kwa munthu amene akumupereka!”+