1 Akorinto 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu? 1 Akorinto 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo atayamika, anaunyemanyema+ n’kunena kuti: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu. Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+
16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?
24 Ndipo atayamika, anaunyemanyema+ n’kunena kuti: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu. Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+