Mateyu 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti wauka kwa akufa,+ moti padakali pano, watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+ Mateyu 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ophunzira 11 aja anapita ku Galileya,+ kuphiri kumene Yesu anakonza kukakumana nawo.
7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti wauka kwa akufa,+ moti padakali pano, watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+