Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+ Maliko 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Petulo anauza Yesu kuti: “Ngakhale ena onse atathawa kukusiyani, koma ine ndekha sindidzatero.”+
2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+
29 Ndiyeno Petulo anauza Yesu kuti: “Ngakhale ena onse atathawa kukusiyani, koma ine ndekha sindidzatero.”+