Maliko 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndithu ndikukuuza, iweyo lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+ Luka 22:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, Tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sundidziwa.”+ Yohane 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, Tambala asanalire undikana katatu.”+
30 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndithu ndikukuuza, iweyo lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+
34 Koma iye anati: “Ndikukuuza iwe Petulo, Tambala asanalire lero, undikana katatu kuti sundidziwa.”+
38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, Tambala asanalire undikana katatu.”+