Maliko 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako anafika pamalo otchedwa Getsemane, ndipo anauza ophunzira akewo kuti: “Khalani pansi pompano, ine ndikukapemphera.”+ Luka 22:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atafika pamalowo anauza ophunzirawo kuti: “Pempherani kosalekeza, kuti musalowe m’mayesero.”+
32 Kenako anafika pamalo otchedwa Getsemane, ndipo anauza ophunzira akewo kuti: “Khalani pansi pompano, ine ndikukapemphera.”+