Mateyu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu+ wanu ubwere. Chifuniro chanu+ chichitike, monga kumwamba, chimodzimodzinso pansi pano.+ Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukusautsika tsopano,+ ndinene chiyani kodi? Atate ndipulumutseni ku nthawi yosautsayi.+ Komabe nthawi imeneyi iyenera kundifikira pakuti ndiye chifukwa chake ndinabwera. Machitidwe 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Titalephera kumusintha maganizo, tinangovomereza ndi kunena kuti: “Chifuniro+ cha Yehova chichitike.”
27 Moyo wanga ukusautsika tsopano,+ ndinene chiyani kodi? Atate ndipulumutseni ku nthawi yosautsayi.+ Komabe nthawi imeneyi iyenera kundifikira pakuti ndiye chifukwa chake ndinabwera.
14 Titalephera kumusintha maganizo, tinangovomereza ndi kunena kuti: “Chifuniro+ cha Yehova chichitike.”