Luka 22:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Yesu pamenepo anafunsa ansembe aakulu, oyang’anira kachisi ndi akulu amene anam’londola kumeneko, kuti: “Bwanji mwabwera ndi malupanga ndi zibonga ngati mukukalimbana ndi wachifwamba?+ Machitidwe 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+
52 Yesu pamenepo anafunsa ansembe aakulu, oyang’anira kachisi ndi akulu amene anam’londola kumeneko, kuti: “Bwanji mwabwera ndi malupanga ndi zibonga ngati mukukalimbana ndi wachifwamba?+
16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+