Maliko 14:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Potsirizira pake, mkulu wa ansembe anaimirira pakati pawo ndi kufunsa Yesu kuti: “Sukuyankha chilichonse? Kodi n’zoona zimene awa akukunenezazi?”+
60 Potsirizira pake, mkulu wa ansembe anaimirira pakati pawo ndi kufunsa Yesu kuti: “Sukuyankha chilichonse? Kodi n’zoona zimene awa akukunenezazi?”+