Luka 22:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Koma iye anakana+ kuti: “Mayi iwe, ameneyu ine sindimudziwa ayi.”+ Yohane 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo mtsikana wantchito, amene anali mlonda wa pakhomopo, anafunsa Petulo kuti: “Kodi inunso si inu mmodzi wa ophunzira a munthu ameneyu?” Iye anati: “Ayi si ine.”+
17 Pamenepo mtsikana wantchito, amene anali mlonda wa pakhomopo, anafunsa Petulo kuti: “Kodi inunso si inu mmodzi wa ophunzira a munthu ameneyu?” Iye anati: “Ayi si ine.”+