Zekariya 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma.+ Zimenezi ndi ndalama za mtengo wapatali zimene akuona kuti angandigule nazo.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo n’kukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+
13 Zitatero Yehova anandiuza kuti: “Kaziponye mosungiramo chuma.+ Zimenezi ndi ndalama za mtengo wapatali zimene akuona kuti angandigule nazo.”+ Choncho ndinatenga ndalama 30 zasilivazo n’kukaziponya mosungiramo chuma panyumba ya Yehova.+