Luka 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano atafika pamalo otchedwa Chibade,+ anamupachika pamenepo pamodzi ndi amuna ochita zoipawo. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+ Yohane 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+
33 Tsopano atafika pamalo otchedwa Chibade,+ anamupachika pamenepo pamodzi ndi amuna ochita zoipawo. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+
17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+