Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Atalowa m’manda achikumbutsowo, anaona mnyamata atakhala pansi kudzanja lamanja, atavala mkanjo woyera, ndipo iwo anadabwa kwambiri.+

  • Luka 24:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Atathedwa nzeru ndi zimenezi, anangoona amuna awiri ovala zovala zonyezimira ataima pambali pawo.+

  • Machitidwe 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mmene iwo anali kuyang’anitsitsa kuthambo pamene iye anali kukwera kumwamba,+ panaonekera amuna awiri ovala zoyera+ ataimirira pambali pawo.

  • Chivumbulutso 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako, ndinaona mngelo+ wina wamphamvu akutsika kuchokera kumwamba, atavala mtambo.+ Kumutu kwake kunali utawaleza, ndipo nkhope yake inali ngati dzuwa.+ Miyendo yake+ inali ngati mizati yamoto.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena