Mateyu 27:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pilato anawayankha kuti: “Inu muli nawo asilikali olondera.+ Pitani kakhwimitseni chitetezo monga mmene mukudziwira.”
65 Pilato anawayankha kuti: “Inu muli nawo asilikali olondera.+ Pitani kakhwimitseni chitetezo monga mmene mukudziwira.”