Mateyu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+ Yohane 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati munthu amandikonda, adzasunga+ mawu anga. Atate wanga adzamukonda, ndipo tidzapita kwa iwo ndi kukakhala nawo.+ 1 Timoteyo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuti usunge lamulolo. Ulisunge uli wopanda banga ndi wopanda chifukwa chokunenezera, kufikira kuonekera+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.
24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+
23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati munthu amandikonda, adzasunga+ mawu anga. Atate wanga adzamukonda, ndipo tidzapita kwa iwo ndi kukakhala nawo.+
14 kuti usunge lamulolo. Ulisunge uli wopanda banga ndi wopanda chifukwa chokunenezera, kufikira kuonekera+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.