1 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye n’zimene inenso ndinakupatsirani, zakuti Ambuye Yesu, usiku+ umene anali kukaperekedwa anatenga mkate. 2 Petulo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti mukumbukire mawu amene aneneri oyera ananena kale,+ ndi lamulo la Ambuye ndi Mpulumutsi wathu kudzera mwa atumwi anu.+ 1 Yohane 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Lamulo lake ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro m’dzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.
23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye n’zimene inenso ndinakupatsirani, zakuti Ambuye Yesu, usiku+ umene anali kukaperekedwa anatenga mkate.
2 kuti mukumbukire mawu amene aneneri oyera ananena kale,+ ndi lamulo la Ambuye ndi Mpulumutsi wathu kudzera mwa atumwi anu.+
23 Lamulo lake ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro m’dzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.